BrandUp Maize Bank ndi kampani za ulimi yomwe imagula chimanga kwa alimi nyengo yokolola mitengo ikatsika. Tagline line yathu ndi "Kuchokera Kumunda Kupita Kumudzi". Vuto lomwe timathetsa ndilakuti alimi ambiri amakakamizika kugulitsa chimanga chawo mwachangu pa mtengo wotsika chifukwa chosowa msika ndi ndalama.pambuyo pake mitengo iimakwera mabanja amavutika ndi njala. Njira yathu ndi yosavuta. Timagula chimanga...