Ndi nd deep freezer 210L kuno kwathu koma ndalama yokwanila kuonjezela business ndili my plan is to get small space kut ndiphika chips nyama and drinks. Koma zikufunika Malo abwino a clean kenako ndikamapeza tima profit ndizipanga zaulimi mbali inayi then ikamatha chaka I know zakhala nd ndalama yokwanila kuzatsegula big restaurant anthu azisadya Malo abwino town yamangochi ino????