1: kugula ti nkhuku ta lokolo pa mtengo otsikirako kumaweta, kumadyetsera Gaga, nsima yotsala komanso zotsala zamatemba zikakula ndikumagulitsa pa mtengo wabwino kuti upeze win. 2: Kugula Njinga ya moto izithamanga pa mseu izikupatsa ndalama tsiku ndi tsiku kuti ngati nkhuku za lokolo zija zitasowa zokudya utha kukagula pa ndalama zomwe yabweretsa njinga ya moto. 3: Kukhala ndi small liquor shop ya budge ya 1million...