Choyamba ulimi wa nkhumba nd ulimi wabwino kwambri utati wapeza breed yabwino kmaso kumanga khola labwino kuti nkhumba zija zizitha kukhala motakasuka bwino ndipameneso zimakula bwino.