Business imenei ndiyabwino kwambiri kwa achinyamata.. Ngati achinyamata mwapanga team yoti muzi painter (ma galimoto ma nyumba etc) ndimbali imodz yothandizirana kupita pa tsogolo ntchito imeneyiyi imangofuna kukhara ndichidwi basi ine kumbali ya ntchito ngati imeneyi ndikupanga business komaso kupanga share kwa luso langa achinyamata anzanga... Ndili ndi anthu ambiri omwe amandifikira kuti ndiziwaphutsi koma...