Business idea yanga ndi STAR HOME MADE/kapena kuti kupanga ma kapani ang'oang'ono womwe azigwirisa ntchito luso popanga ma solution Malawi. Mu star home made Topanga kaguru aka anthu aluso wosiyanasiyana wopanga zithu monga machine wonsayendera magesi wodalira mphavu za Muthu koma zochepa kuti tizipanga zithu wachinsazo: machine wofinya midzimbe kuti madzi ake aturuke wonse ndicholinga choti tipange sugar.Mu Star...