Innocent metal fabrication Works ndi bizinesi ya welding ndi kupanga zinthu zachitsulo yomwe ili ku Mangochi. Timapanga ndi kumanga zitseko zachitsulo zolimba komanso zotsika mtengo, mawindo, zipata, mabenchi, matebulo, ndi mashelufu a m'ma shop a m'nyumba, masukulu, ndi mabizinesi. Komanso ndimakonzanso matanki, zidebe, ndi mipando yachitsulo. Cholinga changa ndikupereka ntchito yabwino yomwe imakhala nthawi...