Ok chofunika ukamayamba business ukuyenela kt uyione kt imapindula bwanji nanga ikufunika zit ndi ziti kt kenako uwone kt izikuthandiza pa moyo wako wa siku ndi siku kenako upange ma bajet a business yomwe ukufunayo ukapamga zimenezozo ubwino wa business uzauziwa ndipo uzaimva kukoma omanso zimafunika ukhale olimba ntima ndi ougwila pandalama choncho business Yako izakula ndikupita pa sogolo kotelo business Yako...