Masikuano zinthu sizikuyenda maka chifukwa chamavuto omwe anthu tikukumana nawo pankhani yazachuma, kotero anthu ambiri tikapedza ndalama choyambilira malingaliro anthu akumakhala pachakudya zina zonse zikumabwera pambuyo. Business yogulitsa zakudya ndi business yokhayo yomwe sikhumudwisa, maka munthu ukakhala waukhondo komanso ukamapedzeka ndichakudya chantundu ulionse. Ine malingaliro ogulitsa zakudya anayamba...