Kuyambitsa famu ya nkhumba zathanzi. Kugulitsa ana a nkhumba. Kuweta nkhumba mpaka kukula ndi kugulitsa. Kupeza ndalama zokhazikika. Kukulitsa chiwerengero cha nkhumba pang’onopang’ono. Kupanga ntchito mtsogolo. Kagwilitsidwe ka ndalama kumanga kapena kukoza makola, kugula mwamkhwala,ku gula chakudya Cha mkhumba , kugula mkhumba zobereketsa