I want to describe in chicMA MA SPARES ANJINGA ZAMOTO Anthu ambiri masiku anthu makamaka achinyamana ambiri akuyendesa njinga zamoto.koma ineyo ndimmodzi mwa achinyamata omwe akukoza njinga zomoto Malawi muno. Koma chifukwa chosowa mpamba ndikulephela kupanga business yomwe ndimaifuna kuyambira kalekale ndimafuna uku ndikukomza kwinaku kumagulisa zisulo zanjingazo Sono business imeneyi imatheka kwambir ngat paliso...