Ndimapanga business ya zovala za muma china zi ndinapeza ka shop of which l pay 50,000 monthly but starting from next month my landrod akuti akufuna akweze from 50,000 to 80,000 koma kwaine ndimmene business ikuyendera panopa sindingakwanitse ndalama yo yandikulila kwambiri coz business yanga sikuti ndiyaikulu ndika small business ndithu what I do is kumzimba kuno ma china shops kulibe tikafuna ma china shops ndiku...