Kuweta nkhuku za mazila ndi business yomwe ndimafuna koma zimakanika chifukwa cha ndalama yoyambira business yo moti apa kuti ndipeze mwayi wa ndalama imeneyo nditha kuweta ndipo ndimazidziwa bwino ndapangapo koma zinali za ayine ake