Business yomwe ndimafuna ndi ya hardware kut zigulisa zipangiza zosiyanasiyana monga zakumunda,zisulo zanjinga ndi zina zambiri.choncho nditha kumakwanisa kuzidalira ndikumapeza thandizo lasiku ndi siku
Agriculture - Startup / Early Operations - Top entries