Kugula makabaza 10. ukhoza kulowetsa K2.5 million ndikupatsa anthu kuti aziyendetsa. patsiku amabweretsa K3,000 ukaipanga masamu pamwezi ndi K750,000 K3,000×25days =K 75,000 K75,000× 10 njinga =K 750,000 Ndet K500,000 yotsalayo kukozera njingazo ngt zina zili ndimavuto Munthu oyendetsayo sadikiraso kuti umulipire amadziripira yekha zimatheka kupeza K10,000 patsiku ndeti apereka K3,000 kwamwini njinga iyeyo K7,000...