Agro Dealer business 1. Kukhalani ndi bizinesi yokhazikika 2. Kukhalani ndi malo okhazikika- kukhala mubizinesi, kuphunzila kuchoka kwa ena, kupangani ndalama 3. Kukula mu bizinesi osuthamangira, kudekha ndikukula pang'onopang'ono. Vuto Chuma cha Malawi chimadalira za ulimi. Ngakhale tili ndi ma agro dealer ena, ndi ochepa ndipo sangathe kukwaniritsa zofuna za anthu. Ambiri mwa iwo ali m'mizinda ndipo ndi ochepa...