Bizinisi ya m’gulu la kagulitsidwe ka katundu (mini retailer shop) komanso yosinthitsa ndi kutumiza ndalama pama foni (mobile money agency). Bizinisi yanga ikuyembekezeka kukhala motere:1. Kagulitsidwe ka Katundu (Mini Retailer Shop)Ichi chikhala sitolo yaing’ono koma yopezeka katundu yense wofunika kwambiri tsiku lililonse pakhomo. Cholinga chake ndichoti anthu a m’dera langa asamayende ulendo wautali...