Ine khumbo langa ndilofuna kusengula malo omwe ndingamapange zo bakery monga cake, bread and many more potengera kuti ndili ndiluso lama phikidwe ndi certificate ya catering, bakery imeneyi ndimafuna izakhale thandizo kwa athu omwe sangakwanise kufikira ntengo wa buledi ma shop chifukwa chakukwera kwa bulediyo. Komaso azakhere malo omwe achinyamata azanga atha kuzapezaso nawo mwayi watchito mudera mwanga . Business...