Mobile Money agent Ndimapanga business imeneyi pano ndikutha chaka ndithu ndipo kwambiri anthu amatenga ndikutumiza ndalama ku Airtel money komaso ku TNM Mpamba ndikugulaso ma units komasoku ma bundle ku Ma Bank amatengaso koma nthw zambiri imakhala month end yokha masiku enawa sikwenikweni ichi zili chonchi chifkwa makamaka anthu ambiri amene amapanga ma business ang'ono ang'ono akamatumizirana ndalama ndalama...