ULIMI WA NKHUMBA. Pig farming ndi ulimi umozi osavuta koma the easiest way to invest in. Ukakhala ndi khola labwino losamalika bwino zimathandizila kut nkhumba zako zichite bwino. Ulimi umenewu ndiwosavuta chifukwa ukhala ndi madzi komaso deya komaso zamasamba ma zomweso ukhoza kungotola kumadimba like ma black jack zosabowolaso thumba. Ulimi wankhumba umakhala easy chifukwa ukhoza kumanga khola lako pafupi ndi...