Business yanga ndiyolima ndikugulitsa mtedza ndikakolora. Of course chaka Chino ndi chachiwiri kukolora koma ndikuonabe tsogolo. Chaka chatha ndinalima half ekara koma ndinakolorabe matumba angapo pakutiso kunali kuyamba koma so pakuti chiyambi ndichovuta koma ndinali okhutitsidwa chaka chino ndinalima ndi kukolora 1 ekara matumba oposera omwe ndinachitira chaka chatha Zomwe zikundipatsa chilimbikitso chopitiliza...