Ndufuna titapanga ulimi wa mtedza komaso business ya zovala izi ndi business zomwe zingathe kusintha moyo wanga mosavuta chifukwa muli phindu silowesa ndalama zambiri mu munda koma phindu limakhalapo ndilambiri komaso business ya zovala ndngathe kupeza ndalama pa siku mosavutaso awa ndima business omwe nduwafuna mu moyo wanga