Kutsegula ma barbershop Kwa Malepera, Kawamba and Chinkhoma trading centres. Kuphatikiza apo kutsegula ma show room Kwa mphamba NDI ku Block 11. Ma business Wawa ndekut ndilemba ntchito anthu five omwe azipindula. Business ya barbershop iliyose ndikuyipatsa K500 000 yomwe ikukwana K1 500 000. Ma video showrooms iliyose K700 000 = K1 400 000. K.100 000 ili padera kutengera kuti ithandize mavuto omwe angadze...