Kuthandiza anthu amudzi mwanthu komaso ozungulira kt asakagulitse mbewu zako kutali kmso kt ikadzafika nthawi yoti azidzagula azidzagula pafupi , business yogula ndikufulitsa zokolora zakumunda ndiyabwino kmso ndiyothandiza miyoyo ya anthu ambiri osat ine ndenkha ndipo ndikhulupirira kt nditachita nawo mwai olandira nawo ndalama imeney ndikhoza kutukula Dera lakwathu kmso ozungulira chifukwa ndikhoza kumathandiza...