Choyamba, Business yanga ndiyogulitsa msaru zama school uniform,ma zip,ulusi osokera, msaru zazovala ngati barbie,Lucas,bridal satin ndizina zokhudza tailoring and designing.komwe ndimakhala kulibe mashop amene amagulitsa zinthu ngati zimenezi kotero anthu ambiri amachoka mmamidzi mutali mutali kupita kumsika wa Msungwi komaso kwamgona kukagula msaru zimene amafuna akapanda kuzipeza amaononga ndrama zambiri kuti...