Business Yanga ndi datrol sculptures yomwe imaumba Komanso kupanga zibolibolipogwiritsa ntchito cement,zitsulo,ma wire,ma plastic Komanso msalu timapanga ziboliboli ndi miphika ma size onse Za mnyumba Komanso tokongoletsera maluwa panja.ziboliboli Za plastic zokutilidwa ndi msalu zimakhala ma size aang'ono ndipo izi zimakhala zokongoletsera mnyumba Komanso timaumba ziboliboli zikulu zikulu zokongoletsera maluwa...