Business yogula ndi kugulitsa mbeu zosiyana siyana monga chimanga ,mtedza,mpunga,ngakhalenso nandolo ndi business yamphindu kwambili ndingoti business yazaulimi ndi business yabwino chifukwa ndi business yokhudza zakudya monga mene mukudziwila athufe Moyo wathu watsiku ndi tsiku ukufunikila kudya.pa 3million pakadali Pano ndi season mene ilili nditha kuwoda mbewu monga mtedza ,chimanga ,nandolo komanso tomato...