Khuku zamazila ndi zabwino kuweta sizivuta kulela kwake bola Ukhale ndi Malo abwino ndikusamala bwino ndiza kudya zake sizisowa. Monga madzi abwino,magetsi Komanso zakudya zoyenela makhwala nthawi yabwino
Support this Builder in Young Builders Challenge Season 2.
One vote per device for this stage.