Business plan yanga yogulitsa msalu (zitenge) Kuno kwathu anthu amavutika kwambiri kuti apeze zitenge ndekuti akuyenela kupita ku mzimba kapena ku mzuzu zomwe ndikutali kwambiri. Nditamagulitsa msalu Kuno nditha kumapanga ndalama kwambiri. Business iyi ndinapangapo koma ndinaduka pazifukwa zina koma ndi business yabwino kwambiri kukhala ndi mpamba wa 3 million kwacha ndi mpamba wa bwino. Kuno chitenje chimodzi ndi...