Choyamba zikufunika kukhala ndi ndalama yokwana at least five hundred thousand ndikupeza madimba 4 1 hector dimba lililose ndikulipila rent dimba limodz sixty thousand ndekut ose pamodzi ikukwana two hundred and fourty thousand Then ndikupeza aganyu akoze madimba ose at least ndalam ingathe kulowa one hundred and fifty thousand then ndikupeza mbewu yochita bwino kwambiri ya mpunga monga kilombelo yomwe simasowa...