Kulima nandolo chinangwa plus chimanga ,nandolo ndi chinangwa utha kulimila pakamoz mmunda mmoz so ukazisamalila bwino utha kupindula,panopa chinangwa Muli ndalama komanso nandolo muli ndalama komanso mbewuzi sizilila zambili zimangofuna chisamalilo basi ,izi zutanthauza kut zilowa zochepa koma zokolola zochuluka