Ndimapanga ulimi waku dimba ndimalima mbewu izi masamba, tomato ndi nyemba.masamba ndikagulisa pa week amatha kundipatsa 20,000 kwacha pamene tomato amatha kundipasa 15,00020,000 kwacha pa week.nyemba zimatha kundipasa 8000 pa week ndikaziika pamodzi zonsezi zimatha kukwana 46 000 pa week.koma ndikachosela ya transport 1500 kupititsa ku msika ndimachosela 10,000 kwacha pa week komanso ndichotsepo yogulira mankhwala...