Ndizigula kuno madeya kukagulitsa ku Zambia ???????? Lusaka,kugula kuno deya thumba ndi 18000, kuphatikizila transport zonse zumakwana 35000 per 50 kg,kugulitsa ku Zambia per 50kg ndi 75000. Malawi chakwa ndekuti ikuwina ndi 49000 malawi kwacha, tikachotsa tikachotsa ma cost amalo ogina ndi chakudya ndekuti ikuwina 25000 per 50 kg imene ili win win kwa ineyo.