Hello,ine ndili ndi business yogulitsa ma grocery,ndimaoda katundu ochepa kutengeraso ndi ndalama ndili nayo yochepa, koma ndikufunitsitsa kut business yangai itakula kut ndizitha ku order katundu ochulukirapo komaso,business yanga ikazakhala yakula ndimafuna ndizalembekoso ntchito anthu ena .