Business yomwe ndikupanga ndi ya kudimba makamaka ya ndiwo za masamba kuphatukizapo anyezi.business ndinaliyamba chifukwa Cha ku Dera kwathu ndiwo zimasowa choncho ndinaganiza kuti anthu asamachita kuyenda mtunda kukasaka ndiwo ndiye ndinachiona chifunika kupeza dimba ndikuyamba kulima masamba,Ndikukamba pano business ya masamba ikutheka ndithu ndadzalanso a nyezi okuti kutsogolo ku anthu azatheso kugula mosavuta...