Ndikhoza umagula mbewu ndikumagulitsanso ku ma company oziwika bwino muno Malawi ngakhaleso mayiko akunja ngati Pali kunthekela kumapititsa mbewu patakhala mwayi otelo komanso business yanga ndikhoza kumayiyang'anila mwachidwi ndicholinga chofuna kt business yanga ipite patsongolo