Kaunjika business ndi business yokagula zovala mitsika ikulu ikulu pa ntengo owoda kapena kukatenga bello mitsika ikulu ikulu . Ndili ndi idea yoti ndisegule shop yot zigulisilamo zovala za belo mostly zachinyamata kutengela kuti mbali zakwathu kuno kuli achinyamata ambili komanso okonda zovala za fashion .