Ineyo ndimalima komano vuto ndi zipangitso moti nditati ndachitika nawo mwayi opata ndalama imeneyi itha kundithandiza pokuza business ya ulimi wanga Maka Maka pokagula , mbewu ya chimanga, 60kgs K776,000, fertilizer chitowe NPK matumba 10×130,000 ndi fertilizer wa Urea 187500×10 komano nd zoti inayo ndtha kuipeza