Kupeza mbewu zakumunda Monga . Nyemba,nkhobwe,nandolo,mtedza, Komanso dzina zongowonjezela Ngati. Mpunga,Ufa, baking frower, mchele, sugar komanso achina soya pices oyezawa ???? ndiyekuti cost yazonsez 2.5m. kenako ndikupanga lent shop ya 150k
Support this Builder in Young Builders Challenge Season 2.
One vote per device for this stage.