Ndimagulitsa katundu ochoka Ku Tanzania ngati; zovala ,masilipasi ndi ma perfume koma sindipita kukatenga Ku Malo omwe amapezekera katundu chifukwa chakusowa mpamba okwanira koma ndimayesesa kukaoda Ku Blantyre limbe(Pacific tower) umu ndi mene business ilipo padakali Pano.