Ndili ndi loto la malonda akugula ndi kugulisa mbeu zakumunda monga; chimanga, nyemba, mpunga, mtedza, soya ndi Zina zatero. Kwathu kuno ndimakhala pansi kuganiza chithu chomwe chingakupitise patsogolo komanso kuthandizira miyoyo ya anthu ena potukula ndikuthana ndi mavuto ena ndi ena ndinawona kuti ndikugula ndi kugulisa mbeu chifukwa mbeu zimathandiza anthu munjira zosiyanasiyana m'moyo wa tsiku ndi tsiku...