If i had a chance to win the money I can start my own business like ya hardware kuyamba ndikuoda oil wamitundu mitundu, then itha kumazipanga yokha grow then ma spares a galimoto pang'ono pang'ono. Iyiyi ndagulitsapo from 2019-2023 . Ndi business yabwino and utha kukwanisa ma bill a monthly with this business