Nditapeza 3milion choyamba nditenga 1milion kukagula ma figuring ana achambo ndikukaponya mu pond yomwe nakumba kale kagula a 750,000 yosala 250,000 kukagula feed then 1milion ina kagula ma piglets 6 akadzi 5 yayimuna imodzi yosarayo yoyambira kugulira zipangizo za feed ndikuyamba kupanga feed ndekha naphuzira kale after that pakusara 1milion ndikuyamba kuweta nkhuku zanyama ñdi madzira feed kumapangaso ndekha...