Maloto anga ndikufuna akupanga shop ndi wholesale business ku Lilongwe yomwe ikupatsa anthu ndi mabizinesi ena katundu wofunikira tsiku ndi tsiku pamtengo wotsika komanso wodalirika. Tiyambila ndi sitolo yogulitsa zinthu monga shuga, mpunga, mafuta, sopo, zakudya, zakumwa, ndi zinthu zina zogwiritsidwa ntchito kunyumba. Tikamakula, tidzakulitsa ntchitoyi kupita ku wholesale kuti tigulitse katundu wambiri kwa eni...