Ndimagulitsa matabwa ku Blantyre. Timagulitsa Zipapati zomangila makola aziweto. Timapereka Zipapati zabwino, owuma bwino, komanso amitengo yotsika. Timathandizanso kudula ndi kutumiza. Ndimagwiritsa ntchito WhatsApp kulankhulana ndi makasitomala.
Support this Builder in Young Builders Challenge Season 2.
One vote per device for this stage.