Ndinayamba business ya nsomba chaka chino mu April, nsomba za ntundu wa chambo ndi damu la plastic lalingono ndi nsomba zokwana 500. Pakadali pano zatha miyez inayi ndikuzisamala, ndimazipatsa chakudya ka wili pa tsiku mammawa ndi madzulo ndipo zikukula ndithu. Ndinayamba ndima fingerlings pano zili nsikhu wa juveniles. Chakudya chake ndimasakaniza ndekha pogwilitsa ntchito mbewu zakumunda ndi blood meal komanso...