Rent Malo ogulisila nkhuku 30000 kuno kwanthu CP kuwoda nkhuku nd 19500 kuigulisa nd 20000 kuiykapo zakudya 50000 kutengera zomwe zizitsala osagulisidwa Ndy kuwoda nkhuku 100 pa, 19,500 nd 1,950,000 ndy kt kugulisa pa 20,000 ukudyapo 500 ndy 500 ×100 nd 50,000 imene ili ndalama yopangidwa patsku ndy pamwez utazipangila kt Uzipuma Sunday osapanga business ndy kt PA mwez uwoda nkhuku masiku 24 Ndy kt 50,000...