Lingaliro la Bizinesi: Njinga 10 za Kabaza Ndili ndi lingaliro la bizinesi logula njinga 10 za kabaza ku Lilongwe. "Kabaza" ndi njira yabwino kwambiri yoyendera anthu kupita Malo osiyanasiyana chifukwa zimafika mwachangu ngakhale m’misewu yaing’ono komanso kudzera munjila zachidule. Kodi bizinesiyo iyenda bwanji? Ndigula njinga 10 zakabaza zatsopano kapena zogwiritsidwa ntchito bwino. Pa njinga iliyonse...