Kugula NDI kugulitsa mbewu NDI business yomwe siimachedwa kutukula munthu wa chidwi Zofunika -Scale yoyezera kachulukidwe (ilipo) -Malo ochitira malonda (alipo osafunikanso ndalama) -Njinga (kapalasa/yamoto) yokanyamulira katundu(mbewu) Chitsanzo :kugula chimanga pa mtengo wa 400Mwk pa kg 400k x 50kg = 20.000k Customer akabwera kudzagula chmanga mtengo NDI 700k 700k x 50kg = 35.000k Total win =15.000k Zimen...