Ndimafuna tayamba business yogulisa mbeu zakumunda monga mpunga,nyemba, mtedza, tomato ndi zina zochokera muthaka. Ndipo nditha kumakaoda Ku kumadera monga ntcheu, dedza, dowa, Kwa jenda ndi ena ozungulira Moti zizatati kuti ziziyenda bwino nditha kumatuluka kunja Kwa dziko lino kukagulitsa mbeu monga ngati Ku Mozambique, Zambia, Tanzania ndi ena ambiri chifukwa business imenei imayenda kwambiri Madera omwe town...